2 Mafumu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Hilikiya mkulu wa ansembe anauza Safani mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la Chilamulo+ mʼnyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani ndipo iye anayamba kuliwerenga.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:8 Nsanja ya Olonda,7/15/1990, tsa. 28
8 Kenako Hilikiya mkulu wa ansembe anauza Safani mlembi+ kuti: “Ndapeza buku la Chilamulo+ mʼnyumba ya Yehova!” Choncho Hilikiya anapereka bukulo kwa Safani ndipo iye anayamba kuliwerenga.+