-
2 Mafumu 23:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Kenako mfumuyo inalamula Hilikiya+ mkulu wa ansembe, ansembe ena ndiponso alonda apakhomo kuti atulutse mʼkachisi wa Yehova ziwiya zonse zimene anapangira Baala, mzati wopatulika*+ ndi gulu lonse la zinthu zakuthambo. Itatero, inakazitentha kunja kwa Yerusalemu pamalo otsetsereka a ku Kidironi ndipo phulusa lake inapita nalo ku Beteli.+
-