2 Mafumu 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mfumuyo inachititsanso kuti ku Tofeti,+ mʼChigwa cha Ana a Hinomu,*+ kukhale kosayenera kulambirako. Inachita zimenezi kuti munthu aliyense asamawotcheko* mwana wake wamwamuna kapena wamkazi pomupereka kwa Moleki.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:10 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 31
10 Mfumuyo inachititsanso kuti ku Tofeti,+ mʼChigwa cha Ana a Hinomu,*+ kukhale kosayenera kulambirako. Inachita zimenezi kuti munthu aliyense asamawotcheko* mwana wake wamwamuna kapena wamkazi pomupereka kwa Moleki.+