-
2 Mafumu 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Komanso mfumuyo inagumula guwa lansembe limene linali ku Beteli ndi malo okwezeka amene Yerobowamu mwana wa Nebati anamanga omwe anachititsa kuti Aisiraeli achimwe.+ Itagwetsa guwa lansembelo komanso malo okwezeka, inatentha malo okwezekawo nʼkuwaperapera mpaka kusanduka fumbi kenako inatenthanso mzati* wopatulika.+
-