2 Mafumu 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anati: “Musakhudze mafupa ake. Asiyeni choncho.” Ndipo iwo sanakhudzedi mafupa akewo komanso mafupa a mneneri amene anachokera ku Samariya.+
18 Iye anati: “Musakhudze mafupa ake. Asiyeni choncho.” Ndipo iwo sanakhudzedi mafupa akewo komanso mafupa a mneneri amene anachokera ku Samariya.+