2 Mafumu 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yosiya anachotsanso akachisi onse a mʼmalo okwezeka amene anali mʼmizinda ya ku Samariya,+ omwe mafumu a Isiraeli anamanga kuti akwiyitse Mulungu. Zimene anachita ndi akachisiwa zinali zofanana ndi zimene anachita ku Beteli.+
19 Yosiya anachotsanso akachisi onse a mʼmalo okwezeka amene anali mʼmizinda ya ku Samariya,+ omwe mafumu a Isiraeli anamanga kuti akwiyitse Mulungu. Zimene anachita ndi akachisiwa zinali zofanana ndi zimene anachita ku Beteli.+