2 Mafumu 23:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iye anapha ansembe onse a mʼmalo okwezeka nʼkuwapereka nsembe pamaguwa ansembe kumeneko. Kenako anawotcha mafupa a anthu pamaguwa ansembewo.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.
20 Iye anapha ansembe onse a mʼmalo okwezeka nʼkuwapereka nsembe pamaguwa ansembe kumeneko. Kenako anawotcha mafupa a anthu pamaguwa ansembewo.+ Atatero anabwerera ku Yerusalemu.