2 Mafumu 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Iye asanakhale mfumu, panalibe mfumu ina imene inabwerera kwa Yehova ndi mtima wake wonse ndi moyo wake wonse+ ndi mphamvu zake zonse, mogwirizana ndi Chilamulo chonse cha Mose. Ndipo pambuyo pake sipanakhalenso mfumu ina ngati iyeyo.
25 Iye asanakhale mfumu, panalibe mfumu ina imene inabwerera kwa Yehova ndi mtima wake wonse ndi moyo wake wonse+ ndi mphamvu zake zonse, mogwirizana ndi Chilamulo chonse cha Mose. Ndipo pambuyo pake sipanakhalenso mfumu ina ngati iyeyo.