2 Mafumu 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova anati: “Yuda nayenso ndidzamʼchotsa pamaso panga+ ngati mmene ndinachotsera Isiraeli+ ndipo ndidzakana mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala kumeneko.’”+
27 Yehova anati: “Yuda nayenso ndidzamʼchotsa pamaso panga+ ngati mmene ndinachotsera Isiraeli+ ndipo ndidzakana mzinda wa Yerusalemu umene ndinausankha, ndi nyumba imene ndinanena kuti, ‘Dzina langa lizikhala kumeneko.’”+