2 Mafumu 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼmasiku ake, Farao Neko mfumu ya Iguputo anapita kukakumana ndi mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate ndipo Mfumu Yosiya, anapita kukamenyana ndi Neko. Koma mfumu ya Iguputoyo itaona Yosiya inamupha ku Megido.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:29 Nsanja ya Olonda,9/15/2000, tsa. 30
29 Mʼmasiku ake, Farao Neko mfumu ya Iguputo anapita kukakumana ndi mfumu ya Asuri pamtsinje wa Firate ndipo Mfumu Yosiya, anapita kukamenyana ndi Neko. Koma mfumu ya Iguputoyo itaona Yosiya inamupha ku Megido.+