2 Mafumu 23:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehoahazi+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 23 ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.
31 Yehoahazi+ anayamba kulamulira ali ndi zaka 23 ndipo analamulira miyezi itatu ku Yerusalemu. Mayi ake anali a ku Libina ndipo dzina lawo linali Hamutali+ mwana wa Yeremiya.