2 Mafumu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Farao Neko+ anamanga Yehoahazi ku Ribila+ mʼdziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Kenako Farao Neko analamula kuti dzikolo lipereke matalente* 100 a siliva ndi talente imodzi ya golide.+
33 Farao Neko+ anamanga Yehoahazi ku Ribila+ mʼdziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Kenako Farao Neko analamula kuti dzikolo lipereke matalente* 100 a siliva ndi talente imodzi ya golide.+