-
2 Mafumu 23:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Yehoyakimu anapereka siliva ndi golide kwa Farao. Koma ankatolera msonkho kwa anthu a mʼdzikolo kuti apereke siliva amene Farao anamulamula. Iye anauza munthu aliyense kuchuluka kwa golide ndi siliva woti azipereka, kuti amupatse Farao Neko.
-