2 Mafumu 24:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:12 Mawu a Mulungu, tsa. 48 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 29
12 Yehoyakini mfumu ya Yuda anapita kwa mfumu ya Babulo+ pamodzi ndi mayi ake, atumiki ake, akalonga ake ndi nduna za panyumba yake+ ndipo mfumu ya Babuloyo inamutenga nʼkupita naye ku ukapolo mʼchaka cha 8 cha ufumu wake.+