2 Mafumu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu ya Babulo inatenganso asilikali onse amphamvu okwana 7,000, amisiri okwana 1,000 komanso anthu osula zitsulo* ndipo onse anali amuna amphamvu komanso ophunzitsidwa kumenya nkhondo nʼkupita nawo ku Babulo.
16 Mfumu ya Babulo inatenganso asilikali onse amphamvu okwana 7,000, amisiri okwana 1,000 komanso anthu osula zitsulo* ndipo onse anali amuna amphamvu komanso ophunzitsidwa kumenya nkhondo nʼkupita nawo ku Babulo.