2 Mafumu 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mfumu ya Babulo inatenga Mataniya, bambo ake aangʼono a Yehoyakini,+ nʼkuwaika kukhala mfumu mʼmalo mwake. Kenako inawasintha dzina kuti akhale Zedekiya.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 29
17 Mfumu ya Babulo inatenga Mataniya, bambo ake aangʼono a Yehoyakini,+ nʼkuwaika kukhala mfumu mʼmalo mwake. Kenako inawasintha dzina kuti akhale Zedekiya.+