-
2 Mafumu 25:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Koma asilikali a Akasidi anayamba kuthamangitsa mfumuyo ndipo anaipeza mʼchipululu cha Yeriko. Zitatero asilikali onse a mfumuyo anabalalika nʼkuisiya yokha.
-