2 Mafumu 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthu amene anatsala mumzindamo, anthu amene anakhala kumbali ya mfumu ya Babulo ndiponso anthu ena onse, nʼkupita nawo ku ukapolo.+
11 Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthu amene anatsala mumzindamo, anthu amene anakhala kumbali ya mfumu ya Babulo ndiponso anthu ena onse, nʼkupita nawo ku ukapolo.+