2 Mafumu 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+
12 Ena mwa anthu osauka kwambiri amʼdzikolo, mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anawasiya kuti akhale olima minda ya mpesa ndi alimi ogwira ntchito mokakamizidwa.+