-
2 Mafumu 25:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu ndi ziwiya zonse zakopa zimene ansembe ankagwiritsa ntchito potumikira mʼkachisi.
-