2 Mafumu 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma sanathe kuyeza kulemera kwa kopa wa zipilala ziwiri zija, thanki yosungira madzi ndiponso zotengera zokhala ndi mawilo zimene Solomo anapanga kuti zizigwira ntchito panyumba ya Yehova.+
16 Koma sanathe kuyeza kulemera kwa kopa wa zipilala ziwiri zija, thanki yosungira madzi ndiponso zotengera zokhala ndi mawilo zimene Solomo anapanga kuti zizigwira ntchito panyumba ya Yehova.+