2 Mafumu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+
21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo ku Ribila mʼdziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anatengedwa kudziko lawo nʼkupita nawo ku ukapolo.+