-
2 Mafumu 25:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Akuluakulu onse a asilikali limodzi ndi asilikali awo atamva kuti mfumu ya Babulo yasankha Gedaliya, nthawi yomweyo anapita kwa Gedaliyayo ku Mizipa. Akuluakuluwo anali Isimaeli mwana wa Netaniya, Yohanani mwana wa Kareya, Seraya mwana wa Tanumeti wa ku Netofa ndiponso Yaazaniya wa ku Maaka, pamodzi ndi asilikali awo.+
-