2 Mafumu 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Gedaliya analumbirira akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kukhala atumiki a Akasidi. Khalani mʼdzikoli nʼkumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.”+
24 Gedaliya analumbirira akuluakuluwo ndi asilikali awo kuti: “Musaope kukhala atumiki a Akasidi. Khalani mʼdzikoli nʼkumatumikira mfumu ya Babulo ndipo zinthu zikuyenderani bwino.”+