2 Mafumu 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mʼmwezi wa 7, Isimaeli+ mwana wa Netaniya mwana wa Elisama, yemwe anali wa kubanja lachifumu* anapita kwa Gedaliya pamodzi ndi amuna 10. Iwo anapha Gedaliya ndi Ayuda ndiponso Akasidi amene anali naye ku Mizipa.+
25 Mʼmwezi wa 7, Isimaeli+ mwana wa Netaniya mwana wa Elisama, yemwe anali wa kubanja lachifumu* anapita kwa Gedaliya pamodzi ndi amuna 10. Iwo anapha Gedaliya ndi Ayuda ndiponso Akasidi amene anali naye ku Mizipa.+