2 Mafumu 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mʼchaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini mfumu ya Yuda,+ Evili-merodaki mfumu ya Babulo anakhala mfumu. Ndiyeno mʼchaka chomwechi mʼmwezi wa 12, pa tsiku la 27 la mweziwo, iye anatulutsa mʼndende Yehoyakini mfumu ya Yuda.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:27 Nsanja ya Olonda,6/1/2012, tsa. 5
27 Mʼchaka cha 37 cha ukapolo wa Yehoyakini mfumu ya Yuda,+ Evili-merodaki mfumu ya Babulo anakhala mfumu. Ndiyeno mʼchaka chomwechi mʼmwezi wa 12, pa tsiku la 27 la mweziwo, iye anatulutsa mʼndende Yehoyakini mfumu ya Yuda.+