2 Mafumu 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma mngelo wa Yehova anauza Eliya*+ wa ku Tisibe kuti: “Pita ukakumane ndi anthu amene atumidwa ndi mfumu ya ku Samariya ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebabu mulungu wa ku Ekironi?+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2138
3 Koma mngelo wa Yehova anauza Eliya*+ wa ku Tisibe kuti: “Pita ukakumane ndi anthu amene atumidwa ndi mfumu ya ku Samariya ndipo ukawafunse kuti, ‘Kodi ku Isiraeli kulibe Mulungu kuti mupite kukafunsa kwa Baala-zebabu mulungu wa ku Ekironi?+