2 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthuwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe ameneyo.” 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:8 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo,
8 Anthuwo anayankha kuti: “Munthuyo anavala chovala chaubweya+ ndi lamba wachikopa mʼchiuno mwake.”+ Mfumuyo itangomva zimenezi, inanena kuti: “Ndi Eliya wa ku Tisibe ameneyo.”