2 Mafumu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto uchokere kumwamba+ ndipo upsereze iweyo ndi asilikali ako 50.” Moto unabweradi kuchokera kumwamba nʼkupsereza mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.
10 Koma Eliya anayankha mtsogoleri wa asilikali 50 uja kuti: “Ngati ndili munthu wa Mulungu, moto uchokere kumwamba+ ndipo upsereze iweyo ndi asilikali ako 50.” Moto unabweradi kuchokera kumwamba nʼkupsereza mtsogoleriyo ndi asilikali ake 50.