-
2 Mafumu 1:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Zitatero mngelo wa Yehova anauza Eliya kuti: “Tsika upite naye limodzi, usamuope.” Choncho Eliya ananyamuka nʼkupita ndi mtsogoleriyo kwa mfumu.
-