2 Mafumu 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako Eliya anauza Elisa kuti: “Iweyo utsale kuno, chifukwa Yehova wandituma ku Beteli.” Koma Elisa anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.” Choncho iwo anapita ku Beteli.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:2 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,4/15/2015, ptsa. 12-138/15/2013, tsa. 29
2 Kenako Eliya anauza Elisa kuti: “Iweyo utsale kuno, chifukwa Yehova wandituma ku Beteli.” Koma Elisa anati: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.” Choncho iwo anapita ku Beteli.+