2 Mafumu 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ana a aneneri* amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa nʼkumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa zimenezo. Khalani chete.”
3 Ndiyeno ana a aneneri* amene anali ku Beteli anabwera kwa Elisa nʼkumufunsa kuti: “Kodi ukudziwa kuti lero Yehova atenga mbuye wako kuti asakhalenso mtsogoleri wako?”+ Iye anayankha kuti: “Ndikudziwa zimenezo. Khalani chete.”