2 Mafumu 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Eliya anauza Elisa kuti: “Elisa, utsale kuno chifukwa Yehova wandituma ku Yeriko.”+ Koma Elisa anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.” Choncho iwo anafika ku Yeriko. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,4/15/2015, ptsa. 12-138/15/2013, tsa. 29
4 Kenako Eliya anauza Elisa kuti: “Elisa, utsale kuno chifukwa Yehova wandituma ku Yeriko.”+ Koma Elisa anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo ndiponso inu muli apa, sindikusiyani.” Choncho iwo anafika ku Yeriko.