2 Mafumu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ ndipo anachipinda nʼkumenya madzi a mumtsinjewo. Madziwo anagawanika uku ndi uku moti iwo anawoloka pouma.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:8 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo,
8 Kenako Eliya anatenga chovala chake chauneneri+ ndipo anachipinda nʼkumenya madzi a mumtsinjewo. Madziwo anagawanika uku ndi uku moti iwo anawoloka pouma.+