2 Mafumu 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atangowoloka, Eliya anauza Elisa kuti: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikuchitire ndisanatengedwe nʼkukusiya.” Elisa anati: “Chonde, ndilandire magawo awiri+ a mzimu wanu.”+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:9 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2013, tsa. 298/1/2005, ptsa. 8-911/1/2003, tsa. 3111/1/1997, tsa. 30
9 Iwo atangowoloka, Eliya anauza Elisa kuti: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikuchitire ndisanatengedwe nʼkukusiya.” Elisa anati: “Chonde, ndilandire magawo awiri+ a mzimu wanu.”+
2:9 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,8/15/2013, tsa. 298/1/2005, ptsa. 8-911/1/2003, tsa. 3111/1/1997, tsa. 30