2 Mafumu 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ankayenda, uku akulankhulana, anangoona galeta* lankhondo lowala ngati moto ndi mahatchi* owala ngati moto.+ Galeta ndi mahatchiwo zinadutsa pakati pawo nʼkuwalekanitsa ndipo Eliya anatengedwa mumphepo yamkuntho nʼkupita kumwamba.*+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:11 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 138/15/2013, ptsa. 29-308/1/2005, tsa. 99/1/2003, tsa. 309/15/1997, tsa. 15
11 Pamene ankayenda, uku akulankhulana, anangoona galeta* lankhondo lowala ngati moto ndi mahatchi* owala ngati moto.+ Galeta ndi mahatchiwo zinadutsa pakati pawo nʼkuwalekanitsa ndipo Eliya anatengedwa mumphepo yamkuntho nʼkupita kumwamba.*+
2:11 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 138/15/2013, ptsa. 29-308/1/2005, tsa. 99/1/2003, tsa. 309/15/1997, tsa. 15