2 Mafumu 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Elisa ankaona zonse zimene zinkachitikazo ndipo ankafuula kuti: “Bambo anga ine! Bambo anga ine! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera mahatchi ake!”+ Elisa ataona kuti Eliya wapita, anagwira zovala zake nʼkuzingʼamba pakati.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo,
12 Elisa ankaona zonse zimene zinkachitikazo ndipo ankafuula kuti: “Bambo anga ine! Bambo anga ine! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera mahatchi ake!”+ Elisa ataona kuti Eliya wapita, anagwira zovala zake nʼkuzingʼamba pakati.+