2 Mafumu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atatero anatola chovala chauneneri+ cha Eliya chimene chinagwa pansi ndipo anabwerera nʼkukaima mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodano.
13 Atatero anatola chovala chauneneri+ cha Eliya chimene chinagwa pansi ndipo anabwerera nʼkukaima mʼmbali mwa mtsinje wa Yorodano.