2 Mafumu 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako anatenga chovala chauneneri cha Eliya chimene chinagwa chija nʼkumenya madzi amumtsinjewo ndipo anati: “Ali kuti Yehova Mulungu wa Eliya?” Atatero madziwo anagawanika ndipo Elisa anawoloka.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, tsa. 13
14 Kenako anatenga chovala chauneneri cha Eliya chimene chinagwa chija nʼkumenya madzi amumtsinjewo ndipo anati: “Ali kuti Yehova Mulungu wa Eliya?” Atatero madziwo anagawanika ndipo Elisa anawoloka.+