-
2 Mafumu 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Elisa atamva zimenezi ananena kuti: “Ndibweretsereni kambale katsopano kolowa ndipo muikemo mchere.” Anthuwo anamʼbweretseradi.
-