2 Mafumu 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo nʼkuponyapo mchere uja+ nʼkunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino ndipo sadzachititsanso imfa kapena kusabereka.’”*
21 Ndiyeno Elisa anapita pamene panayambira madziwo nʼkuponyapo mchere uja+ nʼkunena kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Ndakonza madziwa kuti akhale abwino ndipo sadzachititsanso imfa kapena kusabereka.’”*