2 Mafumu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Elisa ananyamuka nʼkumapita ku Beteli. Ali mʼnjira, anyamata ena a mumzindawo anayamba kumunyoza+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe! Choka kuno wadazi iwe!” 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:23 Nsanja ya Olonda,8/1/2005, tsa. 9
23 Kenako Elisa ananyamuka nʼkumapita ku Beteli. Ali mʼnjira, anyamata ena a mumzindawo anayamba kumunyoza+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe! Choka kuno wadazi iwe!”