2 Mafumu 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako Elisa anatembenuka nʼkuwayangʼana ndipo anawatemberera mʼdzina la Yehova. Ndiyeno zimbalangondo+ ziwiri zazikazi zinatuluka patchire nʼkukhadzula anyamata 42.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:24 Nsanja ya Olonda,11/1/1992, tsa. 9
24 Kenako Elisa anatembenuka nʼkuwayangʼana ndipo anawatemberera mʼdzina la Yehova. Ndiyeno zimbalangondo+ ziwiri zazikazi zinatuluka patchire nʼkukhadzula anyamata 42.+