2 Mafumu 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Elisa anapitiriza ulendo wake ndipo anakafika kuphiri la Karimeli.+ Atachoka kumeneko anabwerera ku Samariya.
25 Elisa anapitiriza ulendo wake ndipo anakafika kuphiri la Karimeli.+ Atachoka kumeneko anabwerera ku Samariya.