2 Mafumu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova, koma osati ngati mmene anachitira bambo ake kapena mayi ake chifukwa anachotsa chipilala chopatulika cha Baala chimene bambo ake anapanga.+
2 Iye ankachita zoipa pamaso pa Yehova, koma osati ngati mmene anachitira bambo ake kapena mayi ake chifukwa anachotsa chipilala chopatulika cha Baala chimene bambo ake anapanga.+