-
2 Mafumu 3:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mesa, yemwe anali mfumu ya Mowabu, anali woweta nkhosa. Ankapereka kwa mfumu ya Isiraeli msonkho wa ana a nkhosa 100,000 ndi nkhosa zamphongo zosameta ubweya zokwana 100,000.
-