2 Mafumu 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wa Yehova kuti tifunsire kwa Yehova kudzera mwa iye?”+ Mtumiki wina wa mfumu ya Isiraeli anayankha kuti: “Kuli Elisa+ mwana wa Safati, amene ankathirira Eliya madzi osamba mʼmanja.”*+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,8/15/2013, ptsa. 28-2911/1/1997, ptsa. 30-31 Tsanzirani, tsa. 98
11 Ndiyeno Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wa Yehova kuti tifunsire kwa Yehova kudzera mwa iye?”+ Mtumiki wina wa mfumu ya Isiraeli anayankha kuti: “Kuli Elisa+ mwana wa Safati, amene ankathirira Eliya madzi osamba mʼmanja.”*+