-
2 Mafumu 3:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Yehosafati atamva zimenezo anati: “Ameneyo ali ndi mawu a Yehova.” Choncho mfumu ya Isiraeli, Yehosafati ndi mfumu ya Edomu anapita kwa Elisa.
-