2 Mafumu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Elisa anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amene ndimamʼtumikira, ndikanakhala kuti sindilemekeza Mfumu Yehosafati+ ya Yuda, sindikanakuyangʼanani nʼkomwe kapena kukusamalani.+
14 Elisa anayankha kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova wa magulu ankhondo akumwamba amene ndimamʼtumikira, ndikanakhala kuti sindilemekeza Mfumu Yehosafati+ ya Yuda, sindikanakuyangʼanani nʼkomwe kapena kukusamalani.+