2 Mafumu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa Yehova wanena kuti: “Simuona mphepo kapena mvula, koma mʼchigwa chonsechi mudzaza madzi.+ Ndipo inu pamodzi ndi ziweto zanu komanso nyama zanu zina mumwa madziwo.”’
17 chifukwa Yehova wanena kuti: “Simuona mphepo kapena mvula, koma mʼchigwa chonsechi mudzaza madzi.+ Ndipo inu pamodzi ndi ziweto zanu komanso nyama zanu zina mumwa madziwo.”’